Levitiko 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tizilombo timene mungadyeto ndi iti: Mtundu uliwonse wa dzombe loyenda mitunda italiitali*+ ndi mitundu ina ya dzombe,+ mtundu uliwonse wa nkhululu, ndi mtundu uliwonse wa chiwala.+
22 Tizilombo timene mungadyeto ndi iti: Mtundu uliwonse wa dzombe loyenda mitunda italiitali*+ ndi mitundu ina ya dzombe,+ mtundu uliwonse wa nkhululu, ndi mtundu uliwonse wa chiwala.+