Ekisodo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula+ dzanja lako ndi kuloza dziko la Iguputo, kuti dzombe ligwe m’dziko lonselo ndi kudya zomera zonse za m’dzikomo, chilichonse chimene matalala anasiya.”+ Miyambo 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Dzombe+ lilibe mfumu koma limauluka lonse litagawikana m’magulumagulu.+ Yesaya 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zimene anthu inu munalanda+ ena zidzasonkhanitsidwa ngati mphemvu zikasonkhana pamodzi, ndiponso ngati chigulu cha dzombe chimene chikukhamukira kwa munthu.+
12 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula+ dzanja lako ndi kuloza dziko la Iguputo, kuti dzombe ligwe m’dziko lonselo ndi kudya zomera zonse za m’dzikomo, chilichonse chimene matalala anasiya.”+
4 Zinthu zimene anthu inu munalanda+ ena zidzasonkhanitsidwa ngati mphemvu zikasonkhana pamodzi, ndiponso ngati chigulu cha dzombe chimene chikukhamukira kwa munthu.+