Yoweli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Amathamanga ngati amuna amphamvu.+ Amakwera khoma ngati amuna ankhondo. Aliyense amayenda m’njira yake ndipo saphonya njira zawo.+
7 “Amathamanga ngati amuna amphamvu.+ Amakwera khoma ngati amuna ankhondo. Aliyense amayenda m’njira yake ndipo saphonya njira zawo.+