2 Samueli 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+
23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+