1 Samueli 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+
18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+