Genesis 44:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Choncho, ndikakangofika kwa kapolo wanu bambo anga, ndilibe mwanayu, amene bambo amam’konda kwambiri ngati mmene amakondera moyo wawo,+ 1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+
30 “Choncho, ndikakangofika kwa kapolo wanu bambo anga, ndilibe mwanayu, amene bambo amam’konda kwambiri ngati mmene amakondera moyo wawo,+
22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+