Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno tsiku lina zinachitika kuti Yonatani+ mwana wa Sauli anauza mtumiki wake womunyamulira zida kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa asilikali a Afilisiti umene uli patsidyapo.” Koma Yonatani sanauze bambo ake zimenezi.+

  • 1 Samueli 14:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ana aamuna a Sauli anali Yonatani,+ Isivi ndi Malikisuwa.+ Ndipo mayina a ana ake awiri aakazi ndi awa: Woyamba kubadwa anali Merabu,+ ndipo wamng’ono anali Mikala.+

  • 2 Samueli 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena