1 Samueli 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+
31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+