21 Inu mapiri a Giliboa,+ musalole kuti mame kapena mvula igwe pa inu. Musalole kuti minda imene ili pa inu ibale zipatso zokaperekedwa kwa Mulungu.+
Chifukwa pa inu chishango cha amuna amphamvu chinadetsedwa,
Chishango cha Sauli, moti palibenso chishango chimene chinadzozedwa ndi mafuta.+