Yoswa 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+ 1 Mafumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anakafunafuna mtsikana wokongola m’dziko lonse la Isiraeli. Pamapeto pake anapeza Abisagi+ Msunemu+ n’kubwera naye kwa mfumu. 2 Mafumu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya. Nyimbo ya Solomo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+ “Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+ “Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.”
3 Ndiyeno anakafunafuna mtsikana wokongola m’dziko lonse la Isiraeli. Pamapeto pake anapeza Abisagi+ Msunemu+ n’kubwera naye kwa mfumu.
8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya.
13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+ “Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+ “Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.”