Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 28:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Afilisiti anasonkhana pamodzi ndi kupita kukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse pamodzi ndi kumanga msasa ku Giliboa.+

  • 1 Mafumu 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno anakafunafuna mtsikana wokongola m’dziko lonse la Isiraeli. Pamapeto pake anapeza Abisagi+ Msunemu+ n’kubwera naye kwa mfumu.

  • 1 Mafumu 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Adoniya anapitiriza kuti: “Chonde, mukauze Mfumu Solomo kuti andipatse Abisagi+ Msunemu+ akhale mkazi wanga. Ndikudziwa kuti inuyo sakakukanirani.”

  • 2 Mafumu 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena