Yoswa 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+ 2 Mafumu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya.
8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza+ Elisa kuti adye chakudya. Nthawi zonse Elisa akamadutsa, anali kupatukira kumeneko kukadya chakudya.