Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 6
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Nyimbo ya Solomo 6:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 45:11; Nym 1:8; 5:9; Chv 19:8

Nyimbo ya Solomo 6:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 5:1
  • +Nym 5:13
  • +Nym 1:7; 2:16

Nyimbo ya Solomo 6:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 7:10; 2Ak 11:2
  • +Yes 40:11; Yoh 10:14; Ahe 13:20

Nyimbo ya Solomo 6:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:9
  • +1Mf 14:17
  • +Sl 48:2; Chv 21:10
  • +Nym 6:10
  • +Sl 20:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, ptsa. 19-20

    11/15/1987, tsa. 25

Nyimbo ya Solomo 6:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:15; 4:9; 7:4
  • +Nym 4:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, tsa. 19

Nyimbo ya Solomo 6:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 4:2

Nyimbo ya Solomo 6:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 4:3

Nyimbo ya Solomo 6:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 11:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2011, tsa. 11

Nyimbo ya Solomo 6:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 2:14
  • +Nym 5:2
  • +Sl 45:9; Yes 49:23

Nyimbo ya Solomo 6:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 8:5; Chv 21:10
  • +2Sa 23:4; Yes 58:8
  • +Yes 24:23
  • +Mt 13:43
  • +Nym 6:4

Nyimbo ya Solomo 6:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani mawu a m’munsi pa Ge 26:17.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mla 2:5; Nym 6:2
  • +De 8:7
  • +Nym 7:12

Nyimbo ya Solomo 6:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 1:10
  • +Nym 1:6; Chv 19:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, tsa. 20

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Nyimbo 6:1Sl 45:11; Nym 1:8; 5:9; Chv 19:8
Nyimbo 6:2Nym 5:1
Nyimbo 6:2Nym 5:13
Nyimbo 6:2Nym 1:7; 2:16
Nyimbo 6:3Nym 7:10; 2Ak 11:2
Nyimbo 6:3Yes 40:11; Yoh 10:14; Ahe 13:20
Nyimbo 6:4Nym 1:9
Nyimbo 6:41Mf 14:17
Nyimbo 6:4Sl 48:2; Chv 21:10
Nyimbo 6:4Nym 6:10
Nyimbo 6:4Sl 20:5
Nyimbo 6:5Nym 1:15; 4:9; 7:4
Nyimbo 6:5Nym 4:1
Nyimbo 6:6Nym 4:2
Nyimbo 6:7Nym 4:3
Nyimbo 6:81Mf 11:1
Nyimbo 6:9Nym 2:14
Nyimbo 6:9Nym 5:2
Nyimbo 6:9Sl 45:9; Yes 49:23
Nyimbo 6:10Nym 8:5; Chv 21:10
Nyimbo 6:102Sa 23:4; Yes 58:8
Nyimbo 6:10Yes 24:23
Nyimbo 6:10Mt 13:43
Nyimbo 6:10Nym 6:4
Nyimbo 6:11Mla 2:5; Nym 6:2
Nyimbo 6:11De 8:7
Nyimbo 6:11Nym 7:12
Nyimbo 6:13Nym 1:10
Nyimbo 6:13Nym 1:6; Chv 19:7
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Nyimbo ya Solomo 6:1-13

Nyimbo ya Solomo

6 “Kodi wachikondi wako wapita kuti, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako walowera kuti, kuti tikuthandize kum’funafuna?”

2 “Wachikondi wanga watsetserekera kumunda wake,+ kumabedi am’munda a maluwa onunkhira,+ kuti akadyetse ziweto+ kuminda, ndiponso kuti akathyole maluwa. 3 Wachikondi wangayo, ine ndine wakewake ndipo iye ndi wangawanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.”

4 “Wokondedwa wangawe, ndiwe wokongola+ ngati Mzinda Wosangalatsa.+ Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+ ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali+ amene azungulira mbendera.+ 5 Yang’ana kumbali kuti maso ako+ asandiyang’anitsitse, chifukwa akundichititsa mantha. Tsitsi lako likuoneka ngati gulu la mbuzi zimene zikudumphadumpha potsetsereka kuchokera ku Giliyadi.+ 6 Mano ako ali ngati gulu la nkhosa zazikazi zimene zikuchokera kozisambitsa, zonse zitabereka mapasa, popanda imene ana ake afa.+ 7 M’mbali mwa mutu wako muli ngati khangaza logamphula pakati, munsalu yako yophimba kumutuyo.+ 8 Pakati pa mafumukazi 60, adzakazi* 80 ndi atsikana osawerengeka,+ 9 pali mmodzi yekha amene ali njiwa yanga,+ wopanda chilema.+ Iye ndiye mwana wamkazi wapadera kwambiri kwa mayi ake. Iyeyo ndi wosadetsedwa kwa mayi amene anam’bereka. Ana aakazi atamuona, anamutcha wodala. Mafumukazi ndi adzakazi anamutamanda+ kuti, 10 ‘Kodi mkazi+ amene akuyang’ana pansi ngati m’bandakuchayu ndani,+ wokongola ngati mwezi wathunthu,+ wosadetsedwa ngati dzuwa lowala,+ wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera?’”+

11 “Ine ndinatsetserekera kumunda+ wa mitengo ya zipatso zokhala ngati mtedza, kuti ndikaone maluwa ake m’chigwa,*+ kuti ndikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira, ndiponso ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+ 12 Mosazindikira, mtima wanga unandifikitsa kumagaleta a anthu olemekezeka a mtundu wanga.”

13 “Bwerera, bwerera iwe Msulami! Bwerera, bwerera kuti tikuone!”+

“Kodi anthu inu mukuona chiyani mwa ine Msulami?”+

“Tikuona ngati tikuonerera gule wa magulu awiri a anthu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena