Nyimbo ya Solomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Wokondedwa wangawe, ndiwe wokongola+ ngati Mzinda Wosangalatsa.+ Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+ ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali+ amene azungulira mbendera.+
4 “Wokondedwa wangawe, ndiwe wokongola+ ngati Mzinda Wosangalatsa.+ Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+ ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali+ amene azungulira mbendera.+