Salimo 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu idzalakalaka kukongola kwako,+Pakuti ndiyo mbuye wako,+Choncho iweramire.+ Nyimbo ya Solomo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ngati iweyo sukudziwa, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse,+ tsatira mapazi a ziweto ndipo ukadyetse ana ako a mbuzi pafupi ndi mahema a abusa.” Nyimbo ya Solomo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+ Chivumbulutso 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+
8 “Ngati iweyo sukudziwa, iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse,+ tsatira mapazi a ziweto ndipo ukadyetse ana ako a mbuzi pafupi ndi mahema a abusa.”
9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+
8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+