Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Nyimbo ya Solomo 5:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 4:16; 6:2
  • +Nym 4:9; 1Ti 5:2
  • +Nym 4:8; Yoh 3:29; Chv 21:9
  • +Nym 4:14
  • +De 26:9; Nym 4:11; Yes 7:15
  • +Nym 1:2, 4

Nyimbo ya Solomo 5:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 3:1
  • +Chv 3:20
  • +Lu 12:36
  • +2Ak 7:1; 11:2; Aef 5:27; 2Pe 3:14; Chv 14:4
  • +Lu 2:8

Nyimbo ya Solomo 5:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 43:30; 1Mf 3:26

Nyimbo ya Solomo 5:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 3:1

Nyimbo ya Solomo 5:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 3:3
  • +Yes 62:6

Nyimbo ya Solomo 5:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 6:13; 10:20
  • +Nym 3:10
  • +Sl 45:2
  • +Nym 2:5

Nyimbo ya Solomo 5:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 45:7
  • +Nym 6:1
  • +Nym 5:8

Nyimbo ya Solomo 5:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 2:52

Nyimbo ya Solomo 5:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2015, tsa. 30

    11/15/2006, tsa. 19

    11/15/1987, tsa. 25

Nyimbo ya Solomo 5:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nym 6:2
  • +Nym 1:13

Nyimbo ya Solomo 5:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, tsa. 19

Nyimbo ya Solomo 5:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 92:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2006, tsa. 19

Nyimbo ya Solomo 5:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 45:2; Nym 2:3

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Nyimbo 5:1Nym 4:16; 6:2
Nyimbo 5:1Nym 4:9; 1Ti 5:2
Nyimbo 5:1Nym 4:8; Yoh 3:29; Chv 21:9
Nyimbo 5:1Nym 4:14
Nyimbo 5:1De 26:9; Nym 4:11; Yes 7:15
Nyimbo 5:1Nym 1:2, 4
Nyimbo 5:2Nym 3:1
Nyimbo 5:2Chv 3:20
Nyimbo 5:2Lu 12:36
Nyimbo 5:22Ak 7:1; 11:2; Aef 5:27; 2Pe 3:14; Chv 14:4
Nyimbo 5:2Lu 2:8
Nyimbo 5:4Ge 43:30; 1Mf 3:26
Nyimbo 5:6Nym 3:1
Nyimbo 5:7Nym 3:3
Nyimbo 5:7Yes 62:6
Nyimbo 5:8De 6:13; 10:20
Nyimbo 5:8Nym 3:10
Nyimbo 5:8Sl 45:2
Nyimbo 5:8Nym 2:5
Nyimbo 5:9Sl 45:7
Nyimbo 5:9Nym 6:1
Nyimbo 5:9Nym 5:8
Nyimbo 5:10Lu 2:52
Nyimbo 5:13Nym 6:2
Nyimbo 5:13Nym 1:13
Nyimbo 5:15Sl 92:12
Nyimbo 5:16Sl 45:2; Nym 2:3
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Nyimbo ya Solomo 5:1-16

Nyimbo ya Solomo

5 “Ndabwera m’munda mwanga,+ iwe mlongo wanga,+ mkwatibwi wanga.+ Ndathyola mule+ wanga limodzi ndi zonunkhiritsa zanga. Ndadya chisa changa cha uchi limodzi ndi uchi wanga.+ Ndamwa vinyo wanga limodzi ndi mkaka wanga.”

“Idyani, inu anthu okondana! Imwani ndipo muledzere ndi chikondi chimene mukusonyezana.”+

2 “Panopa ndili m’tulo koma mtima wanga uli maso.+ Ndikumva wachikondi wanga akugogoda.”+

“Nditsegulire+ iwe mlongo wanga, wokondedwa wanga, njiwa yanga, iwe wopanda chilema.+ Pakuti m’mutu mwanga mwadzaza mame, ndipo tsitsi langa ladzaza madontho a madzi a usiku.”+

3 “‘Ndavula mkanjo wanga. Kodi ndiuvalenso? Ndatsuka mapazi anga. Kodi ndiwadetsenso?’ 4 Wachikondi wanga atachotsa dzanja lake pabowo la chitseko, m’mimba mwanga+ munabwadamuka. 5 Ine ndinadzuka kuti ndimutsegulire wachikondi wanga ndipo manja anga anali kuyenderera mafuta a mule. Zala zanga zinali kuyenderera mule pamene ndinali kugwira pabowo lolowetsapo loko wa pachitseko. 6 Ndinam’tsegulira wachikondi wanga, koma wachikondi wangayo anali atachokapo, atapita. Moyo wanga unachoka mwa ine nditamva mawu ake. Ndinam’funafuna koma sindinam’peze.+ Ndinamuitana koma sanandiyankhe. 7 Alonda+ amene anali kuyendayenda mumzinda anandipeza. Anandimenya, anandivulaza. Alonda a pamipanda+ anandilanda chofunda changa.

8 “Ndakulumbiritsani+ inu ana aakazi a ku Yerusalemu+ kuti mukam’peza wachikondi wanga,+ mumuuze kuti ine chikondi chikundidwalitsa.”+

9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+

10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+ 11 Mutu wake ndi wokongola ngati golide, golide woyengedwa bwino. Tsitsi lake lili ngati zipatso za kanjedza. Tsitsi lakelo ndi lakuda ngati khwangwala. 12 Maso ake ali ngati njiwa zimene zili pafupi ndi mtsinje wamadzi, zimene zikusamba mumkaka, zitakhala chakumphepete kwa madziwo. 13 Masaya ake ali ngati bedi la m’munda la maluwa onunkhira,+ ndiponso ngati nsanja zomangidwa ndi zitsamba zonunkhira. Milomo yake ili ngati maluwa amene akuchucha mafuta a mule.+ 14 Zala zake zonenepa bwino ndi zagolide, ndipo zikhadabo zake ndi zakulusolito. Mimba yake ndi yopangidwa ndi minyanga ya njovu yokutidwa ndi miyala ya safiro. 15 Miyendo yake ili ngati zipilala zamiyala ya mabo zozikidwa pazitsulo zokhala ndi mphako, zagolide woyengedwa bwino. Iye ndi wokongola ngati dziko la Lebanoni ndipo palibe wofanana naye pa nkhani ya kukongola, mofanana ndi mitengo ya mkungudza.+ 16 M’kamwa mwake ndi mokoma kwambiri ndipo chilichonse mwa iye n’chosiririka.+ Ameneyu ndiye wachikondi wanga ndipo ameneyutu ndiye wokondedwa wanga, inu ana aakazi a ku Yerusalemu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena