Nyimbo ya Solomo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dzuka, iwe mphepo yakumpoto. Bwera, iwe mphepo yakum’mwera.+ Womba pamunda wanga+ kuti kununkhira kwake kumveke.” “Wachikondi wanga alowe m’munda wake kuti adzadye zipatso zake zokoma kwambiri.” Nyimbo ya Solomo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Wachikondi wanga watsetserekera kumunda wake,+ kumabedi am’munda a maluwa onunkhira,+ kuti akadyetse ziweto+ kuminda, ndiponso kuti akathyole maluwa.
16 Dzuka, iwe mphepo yakumpoto. Bwera, iwe mphepo yakum’mwera.+ Womba pamunda wanga+ kuti kununkhira kwake kumveke.” “Wachikondi wanga alowe m’munda wake kuti adzadye zipatso zake zokoma kwambiri.”
2 “Wachikondi wanga watsetserekera kumunda wake,+ kumabedi am’munda a maluwa onunkhira,+ kuti akadyetse ziweto+ kuminda, ndiponso kuti akathyole maluwa.