Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nyimbo ya Solomo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tiye tichokere limodzi ku Lebanoni, iwe mkwatibwi wanga,+ tiye tichoke ku Lebanoni.+ Utsetsereke kuchokera pamwamba pa phiri la Amana, kuchokera pamwamba pa phiri la Seniri,+ ngakhalenso pamwamba pa phiri la Herimoni.+ Utsetsereke kuchokera m’mapanga a mikango, ndiponso kuchokera kumapiri a akambuku.*

  • Yohane 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iye amene ali ndi mkwatibwi ndiye mkwati.+ Koma mnzake wa mkwati, akaimirira ndi kumvetsera zimene akunena, amakhala n’chimwemwe chochuluka chifukwa cha mawu a mkwatiyo. Choncho chimwemwe changa chasefukiradi.+

  • Chivumbulutso 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo kunabwera mmodzi wa angelo 7 aja, amene anali ndi mbale 7 zodzaza ndi miliri+ 7 yotsiriza. Iye anandiuza kuti: “Bwera kuno ndikuonetse mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena