Chivumbulutso 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taona! Ndaima pakhomo,+ ndipo ndikugogoda. Wina akamva mawu anga ndi kutsegula chitseko,+ ndidzalowa m’nyumba mwake ndipo iye ndi ine tidzadyera limodzi chakudya chamadzulo.
20 Taona! Ndaima pakhomo,+ ndipo ndikugogoda. Wina akamva mawu anga ndi kutsegula chitseko,+ ndidzalowa m’nyumba mwake ndipo iye ndi ine tidzadyera limodzi chakudya chamadzulo.