Deuteronomo 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno anatibweretsa kumalo ano ndi kutipatsa dziko ili, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Nyimbo ya Solomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Milomo yako imangokhalira kukha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi+ ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako, ndipo kununkhira kwa zovala zako kuli ngati kununkhira+ kwa nkhalango ya Lebanoni. Yesaya 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye azidzadya mafuta a mkaka ndi uchi pofika nthawi imene adzadziwe kukana choipa ndi kusankha chabwino.+
11 Milomo yako imangokhalira kukha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi+ ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako, ndipo kununkhira kwa zovala zako kuli ngati kununkhira+ kwa nkhalango ya Lebanoni.
15 Iye azidzadya mafuta a mkaka ndi uchi pofika nthawi imene adzadziwe kukana choipa ndi kusankha chabwino.+