Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+ Luka 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndipo mwanayo anali kukulirakulira ndi kukhala wamphamvu.+ Nzeru zake zinali kuchuluka ndipo Mulungu anapitiriza kukondwera naye.+ Aroma 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chikondi+ chanu chisakhale cha chiphamaso.+ Nyansidwani ndi choipa,+ gwiritsitsani chabwino.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
40 Ndipo mwanayo anali kukulirakulira ndi kukhala wamphamvu.+ Nzeru zake zinali kuchuluka ndipo Mulungu anapitiriza kukondwera naye.+