Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+