Salimo 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kondani Yehova, inu nonse okhulupirika ake.+Yehova amateteza okhulupirika,+Koma aliyense wodzikuza adzamulanga mowirikiza.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+ Salimo 145:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amayang’anira onse omukonda,+Koma oipa onse adzawafafaniza.+ Miyambo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 mwa kuyang’anitsitsa njira zachiweruzo,+ ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+
23 Kondani Yehova, inu nonse okhulupirika ake.+Yehova amateteza okhulupirika,+Koma aliyense wodzikuza adzamulanga mowirikiza.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+