Yobu 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana ake akachuluka, amachulukira lupanga.+Mbadwa zake sizidzakhala ndi chakudya chokwanira. Salimo 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzawononga ana awo kuwachotsa padziko lapansi,+Ndipo ana awo mudzawachotsa pakati pa ana a anthu.+ Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+
10 Mudzawononga ana awo kuwachotsa padziko lapansi,+Ndipo ana awo mudzawachotsa pakati pa ana a anthu.+