Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+ Salimo 104:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ochimwa adzafafanizidwa padziko lapansi.+Ndipo anthu oipa sadzakhalaponso.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Tamandani Ya, anthu inu!*+ Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+
20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+
35 Ochimwa adzafafanizidwa padziko lapansi.+Ndipo anthu oipa sadzakhalaponso.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Tamandani Ya, anthu inu!*+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+