Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma oipa onse adzatheratu,+Adani a Yehova adzasowa mofulumira ngati malo okongola odyetsera ziweto amene msipu wake wobiriwira suchedwa kufota.Iwo adzatha mofulumira ngati utsi.
20 Koma oipa onse adzatheratu,+Adani a Yehova adzasowa mofulumira ngati malo okongola odyetsera ziweto amene msipu wake wobiriwira suchedwa kufota.Iwo adzatha mofulumira ngati utsi.