Salimo 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+
20 Pakuti anthu oipa adzatheratu onse,+Ndipo adani a Yehova adzafanana ndi busa la msipu wobiriwira mochititsa kaso.Iwo adzatha.+ Adzazimiririka ndi kusanduka utsi.+