Salimo 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anthu onse ochimwa adzafafanizidwa.+M’tsogolo, anthu oipa adzaphedwa.+ Salimo 101:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa uliwonse ndidzawononga oipa onse a padziko lapansi.+Ndidzapha ndi kuchotsa mumzinda wa Yehova anthu onse ochita zinthu zopweteka anzawo.+ Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+
8 M’mawa uliwonse ndidzawononga oipa onse a padziko lapansi.+Ndidzapha ndi kuchotsa mumzinda wa Yehova anthu onse ochita zinthu zopweteka anzawo.+