Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+ Salimo 109:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+
5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+
15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+