Salimo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+ Yesaya 65:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu inu mudzasiya dzina lanu kuti anthu anga osankhidwa mwapadera aziligwiritsa ntchito potemberera ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzakuphani mmodzi ndi mmodzi,+ koma atumiki ake adzawapatsa dzina lina.+
16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+
15 Anthu inu mudzasiya dzina lanu kuti anthu anga osankhidwa mwapadera aziligwiritsa ntchito potemberera ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzakuphani mmodzi ndi mmodzi,+ koma atumiki ake adzawapatsa dzina lina.+