Yesaya 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako+ mkazi iwe,+ ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzatchedwa ndi dzina latsopano+ limene pakamwa pa Yehova padzasankhe. Yeremiya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’masiku amenewo, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu adzatchedwa kuti, Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.’”+ Aroma 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo pamalo pamene anauzidwapo kuti, ‘Inu sindinu anthu anga,’ pamalo omwewo adzatchedwa ‘ana a Mulungu wamoyo.’”+
2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako+ mkazi iwe,+ ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzatchedwa ndi dzina latsopano+ limene pakamwa pa Yehova padzasankhe.
16 M’masiku amenewo, Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu adzatchedwa kuti, Yehova Ndiye Chilungamo Chathu.’”+
26 Ndipo pamalo pamene anauzidwapo kuti, ‘Inu sindinu anthu anga,’ pamalo omwewo adzatchedwa ‘ana a Mulungu wamoyo.’”+