Yesaya 48:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Sonkhanani pamodzi anthu nonsenu kuti mumve.+ Ndani pakati pawo ananenapo zinthu zimenezi? Iye amene Yehova wamukonda+ adzachitira Babulo zimene akufuna.+ Dzanja lake lidzakhala pa Akasidi.+ Yesaya 54:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe udzakhazikika m’chilungamo.+ Kuponderezedwa udzatalikirana nako,+ ndipo sudzaopa aliyense. Chilichonse choopsa udzatalikirana nacho, pakuti sichidzakuyandikira.+ Yohane 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo iye akadzafika adzapereka umboni wotsimikizika ku dzikoli wonena za tchimo, za chilungamo, ndi za chiweruzo.+
14 “Sonkhanani pamodzi anthu nonsenu kuti mumve.+ Ndani pakati pawo ananenapo zinthu zimenezi? Iye amene Yehova wamukonda+ adzachitira Babulo zimene akufuna.+ Dzanja lake lidzakhala pa Akasidi.+
14 Iwe udzakhazikika m’chilungamo.+ Kuponderezedwa udzatalikirana nako,+ ndipo sudzaopa aliyense. Chilichonse choopsa udzatalikirana nacho, pakuti sichidzakuyandikira.+
8 Ndipo iye akadzafika adzapereka umboni wotsimikizika ku dzikoli wonena za tchimo, za chilungamo, ndi za chiweruzo.+