Yohane 12:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Aliyense wondinyalanyaza ndi kusalandira mawu anga, ali naye mmodzi womuweruza. Mawu+ amene ine ndalankhula ndi amene adzamuweruze pa tsiku lomaliza. Machitidwe 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pamene anali kulankhula za chilungamo,+ za kudziletsa,+ ndi za chiweruzo+ chimene chikudzacho, Felike anachita mantha ndipo anayankha kuti: “Basi, padakali pano ungapite, ndikadzapeza nthawi ndidzakuitananso.”
48 Aliyense wondinyalanyaza ndi kusalandira mawu anga, ali naye mmodzi womuweruza. Mawu+ amene ine ndalankhula ndi amene adzamuweruze pa tsiku lomaliza.
25 Koma pamene anali kulankhula za chilungamo,+ za kudziletsa,+ ndi za chiweruzo+ chimene chikudzacho, Felike anachita mantha ndipo anayankha kuti: “Basi, padakali pano ungapite, ndikadzapeza nthawi ndidzakuitananso.”