Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 24
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 24:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:2
  • +Mac 25:2, 15
  • +Mac 23:26

Machitidwe 24:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 12:2; 55:21; Miy 26:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 192

Machitidwe 24:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 192

Machitidwe 24:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:11; Mac 16:20; 17:6
  • +Lu 23:2; Mac 19:40
  • +Mt 2:23; Mac 28:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 192

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2001, ptsa. 22-23

Machitidwe 24:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 192

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2001, ptsa. 22-23

Machitidwe 24:7

Mawu a M'munsi

  • *

    Za mawu amene palibe, onani mawu a m’munsi pa Mt 17:21.

Machitidwe 24:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 3:15

Machitidwe 24:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:26

Machitidwe 24:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 25:8
  • +Mac 21:28

Machitidwe 24:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 25:7

Machitidwe 24:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 3:15; Mac 3:13; 26:22; 2Ti 1:3
  • +De 18:18; Mac 28:23; Aro 3:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 13-14

Machitidwe 24:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:6
  • +Yes 26:19; Da 12:2; Mt 22:31; Yoh 5:28; 11:25; Chv 20:12
  • +Lu 14:14; Ahe 11:35
  • +Lu 23:43

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, ptsa. 16-17, 20, 22, 26

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 30

    Galamukani!,

    No. 1 2021 tsa. 13

    9/8/1990, ptsa. 26-27

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 7

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/2015, tsa. 6

    6/1/2014, ptsa. 10-11

    3/15/2012, tsa. 11

    6/15/2006, tsa. 6

    7/15/2001, tsa. 6

    7/15/2000, ptsa. 13-14

    4/1/1999, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 22

    2/15/1995, ptsa. 8-12

    8/1/1991, tsa. 6

    5/1/1990, tsa. 26

    Zimene Baibulo Limaphunzitsa, ptsa. 77-79

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, ptsa. 72-73

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 297-298

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 170-172, 179-180

    Kukambitsirana, ptsa. 113, 293

Machitidwe 24:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 6:5; Mac 23:1; 1Ak 4:4; Ahe 13:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2005, ptsa. 14-15

Machitidwe 24:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:29; 2Ak 8:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 169

Machitidwe 24:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:26

Machitidwe 24:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:30; 25:16

Machitidwe 24:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:6; 28:20

Machitidwe 24:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:24
  • +Mac 9:2; 19:9
  • +Mac 23:26

Machitidwe 24:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 27:3

Machitidwe 24:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:24
  • +Mac 16:1
  • +Mt 10:18; 1Pe 3:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 194-195

Machitidwe 24:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 1:17; 3:22
  • +Aga 5:23; 2Pe 1:6
  • +Mt 12:18; Yoh 16:8; 2Ak 5:10; Chv 20:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 194-195

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/1993, ptsa. 17-19

Machitidwe 24:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 23:8; De 16:19; Sl 26:10; Miy 17:23; Yes 5:23
  • +Mko 6:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2001, tsa. 23

Machitidwe 24:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 29:25; Lu 23:25; Mac 25:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 195

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 24:1Mac 23:2
Mac. 24:1Mac 25:2, 15
Mac. 24:1Mac 23:26
Mac. 24:2Sl 12:2; 55:21; Miy 26:28
Mac. 24:3Mac 23:26
Mac. 24:5Mt 5:11; Mac 16:20; 17:6
Mac. 24:5Lu 23:2; Mac 19:40
Mac. 24:5Mt 2:23; Mac 28:22
Mac. 24:6Mac 21:28
Mac. 24:101Pe 3:15
Mac. 24:11Mac 21:26
Mac. 24:12Mac 25:8
Mac. 24:12Mac 21:28
Mac. 24:13Mac 25:7
Mac. 24:14Eks 3:15; Mac 3:13; 26:22; 2Ti 1:3
Mac. 24:14De 18:18; Mac 28:23; Aro 3:21
Mac. 24:15Mac 23:6
Mac. 24:15Yes 26:19; Da 12:2; Mt 22:31; Yoh 5:28; 11:25; Chv 20:12
Mac. 24:15Lu 14:14; Ahe 11:35
Mac. 24:15Lu 23:43
Mac. 24:16Da 6:5; Mac 23:1; 1Ak 4:4; Ahe 13:18
Mac. 24:17Mac 11:29; 2Ak 8:4
Mac. 24:18Mac 21:26
Mac. 24:19Mac 23:30; 25:16
Mac. 24:21Mac 23:6; 28:20
Mac. 24:22Mac 23:24
Mac. 24:22Mac 9:2; 19:9
Mac. 24:22Mac 23:26
Mac. 24:23Mac 27:3
Mac. 24:24Mac 23:24
Mac. 24:24Mac 16:1
Mac. 24:24Mt 10:18; 1Pe 3:15
Mac. 24:25Aro 1:17; 3:22
Mac. 24:25Aga 5:23; 2Pe 1:6
Mac. 24:25Mt 12:18; Yoh 16:8; 2Ak 5:10; Chv 20:12
Mac. 24:26Eks 23:8; De 16:19; Sl 26:10; Miy 17:23; Yes 5:23
Mac. 24:26Mko 6:20
Mac. 24:27Miy 29:25; Lu 23:25; Mac 25:9
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 24:1-27

Machitidwe

24 Patapita masiku asanu, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula, dzina lake Teritulo. Iwo ananeneza+ Paulo kwa bwanamkubwa.+ 2 Teritulo atapatsidwa mwayi kuti alankhulepo, anayamba kuneneza Paulo. Iye anati:

“Tili pa mtendere wochuluka+ chifukwa cha inu, komanso zinthu zikusintha mu mtundu wathuwu chifukwa cha nzeru zanu zoona patali. 3 Choncho nthawi zonse komanso kulikonse, Inu Wolemekezeka+ a Felike, ife timayamikira kwambiri kulandira nzeru zanuzo. 4 Koma kuti ndisakutayitseni nthawi, ndikupempha chonde kuti mumve mawu athu pang’ono, mwa kukoma mtima kwanu. 5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+ 6 Iyeyu anayesanso kudetsa kachisi,+ ndipo tinamugwira. 7* —— 8 Mutamufunsa, mungathe kutsimikizira nokha zonse zimene tikumunenezazi.”

9 Atanena zimenezi Ayuda nawonso analowerera kumuukira. Iwo anali kunena motsindika kuti zimenezo n’zoonadi. 10 Pamene bwanamkubwayo anagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti:

“Ine podziwa bwino kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri, ndine wokondwa kuti ndilankhule podziteteza+ pa zimene akundinenezazi. 11 Inu mukhoza kupeza umboni wakuti sipanapite masiku 12 kuchokera pamene ine ndinapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu.+ 12 Ndipo iwowa sanandipezepo m’kachisi+ ndikutsutsana ndi wina aliyense, ngakhale kuyambitsa chipolowe+ m’masunagoge kapena pena paliponse mumzindawu. 13 Ngakhalenso panopa sangathe kukupatsani umboni+ wa zimene akundinenezazi. 14 Komatu ndikuvomereza izi kwa inu: Njira yolambirira imene iwo akuitcha ‘gulu lampatuko,’ ndi njira imene ine ndikuchitira utumiki wopatulika kwa Mulungu wa makolo anga.+ Pakuti ndimakhulupirira zonse zimene zili m’Chilamulo+ ndi Zolemba za aneneri. 15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+ 16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu. 17 Choncho pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapatsa mtundu wanga mphatso zachifundo, ndiponso kudzapereka nsembe.+ 18 Pamene ndinali kuchita zimenezi, anandipeza m’kachisi nditadziyeretsa monga mwa mwambo,+ koma panalibe khamu la anthu kapena wochita phokoso. Kumeneko kunali Ayuda ena ochokera m’chigawo cha Asia. 19 Amenewo ndiwo anali oyenera kupezeka pano pamaso panu kudzandineneza ine akanakhala ndi chifukwa chondiimbira mlandu.+ 20 Kapena, muwalole anthu ali panowa, afotokoze okha ngati anandipeza ndi cholakwa chilichonse pamene ndinaimirira pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. 21 Mawu amodzi okha amene ine ndinafuula, pamene ndinaimirira pakati pawo ndi akuti, ‘Ine lero ndikuweruzidwa pamaso panu chifukwa cha nkhani ya kuuka kwa akufa!’”+

22 Komabe Felike,+ ankadziwa bwino kwambiri nkhani yokhudza Njira imeneyi,+ choncho anaimitsa mlanduwo ndi kunena kuti: “Ndidzagamula mlandu wanuwu akadzafika Lusiya+ mkulu wa asilikali.” 23 Choncho analamula kapitawo wa asilikali kuti amuyang’anire munthuyu ndi kumupatsako ufulu, ndi kuti asaletse munthu aliyense mwa anthu a mtundu wake kumutumikira.+

24 Patapita masiku angapo, Felike+ anafika pamodzi ndi mkazi wake Durusila, amene anali mayi wachiyuda.+ Choncho Felike anaitanitsa Paulo ndi kumumvetsera pamene anali kufotokoza za kukhulupirira Khristu Yesu.+ 25 Koma pamene anali kulankhula za chilungamo,+ za kudziletsa,+ ndi za chiweruzo+ chimene chikudzacho, Felike anachita mantha ndipo anayankha kuti: “Basi, padakali pano ungapite, ndikadzapeza nthawi ndidzakuitananso.” 26 Pa nthawi imodzimodziyo, anali kuyembekezera kuti Paulo amupatse ndalama.+ Pa chifukwa chimenechi anali kumuitanitsa kawirikawiri n’kumakambirana naye.+ 27 Koma zaka ziwiri zitatha, Felike anachoka ndipo Porikiyo Fesito ndi amene analowa m’malo mwake. Koma popeza kuti Felike ankafuna kuti Ayuda azimukonda,+ anangomusiya m’ndende Paulo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena