Machitidwe 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa. Machitidwe 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ena anapitiriza kuumitsa mitima yawo osakhulupirira,+ ndipo anali kunena zonyoza Njirayo+ pamaso pa khamu la anthu. Choncho iye anawachokera+ n’kuchotsanso ophunzirawo pakati pawo.+ Ndipo tsiku ndi tsiku anali kukamba nkhani m’holo pasukulu ya Turano.
2 kukamupempha zikalata za chilolezo zopita nazo kumasunagoge a ku Damasiko. Anapempha zikalatazo kuti akakapeza wina aliyense wotsatira Njirayo,*+ mwamuna kapena mkazi, akabwere naye ku Yerusalemu ali womangidwa.
9 Koma ena anapitiriza kuumitsa mitima yawo osakhulupirira,+ ndipo anali kunena zonyoza Njirayo+ pamaso pa khamu la anthu. Choncho iye anawachokera+ n’kuchotsanso ophunzirawo pakati pawo.+ Ndipo tsiku ndi tsiku anali kukamba nkhani m’holo pasukulu ya Turano.