Mateyu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, potuluka m’nyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo sansani fumbi kumapazi anu.+ Aroma 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+
14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, potuluka m’nyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo sansani fumbi kumapazi anu.+
17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+