Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kulikonse kumene sakakulandirani kapena kukumvetserani, pochoka kumeneko sansani fumbi kumapazi anu kuti ukhale umboni kwa iwo.”+

  • Luka 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo ngati pakhomopo pali munthu wokonda mtendere, mtendere wanu udzakhala pa iye.+ Koma ngati palibe, udzabwerera kwa inu.+

  • Luka 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ‘Ngakhale fumbi la mumzinda wanu uno, limene lamamatira kumapazi kwathu, tikukusansirani.+ Komabe, kumbukirani kuti, ufumu wa Mulungu wayandikira.’

  • Machitidwe 13:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Koma Paulo ndi Baranaba anasansira anthuwo fumbi kumapazi awo+ n’kupita ku Ikoniyo.

  • Machitidwe 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena