Mateyu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, potuluka m’nyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo sansani fumbi kumapazi anu.+ Machitidwe 13:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Koma Paulo ndi Baranaba anasansira anthuwo fumbi kumapazi awo+ n’kupita ku Ikoniyo.
14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, potuluka m’nyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo sansani fumbi kumapazi anu.+