Mateyu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, potuluka m’nyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo sansani fumbi kumapazi anu.+ Luka 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kulikonse kumene anthu sakakulandirani, potuluka mumzinda+ umenewo, sansani fumbi kumapazi anu kuti ukhale umboni wowatsutsa.”+ Machitidwe 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+
14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, potuluka m’nyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo sansani fumbi kumapazi anu.+
5 Kulikonse kumene anthu sakakulandirani, potuluka mumzinda+ umenewo, sansani fumbi kumapazi anu kuti ukhale umboni wowatsutsa.”+
6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+