Machitidwe 13:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Chotero Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Kunali koyenera kuti inu mukhale oyamba kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza kuti mukuwatayira kumbali+ ndipo mukudziweruza nokha kukhala osayenera moyo wosatha, ifeyo tikutembenukira kwa anthu a mitundu ina.+ Machitidwe 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+ Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+
46 Chotero Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Kunali koyenera kuti inu mukhale oyamba kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza kuti mukuwatayira kumbali+ ndipo mukudziweruza nokha kukhala osayenera moyo wosatha, ifeyo tikutembenukira kwa anthu a mitundu ina.+
28 Chotero dziwani kuti njira ya Mulungu yopulumutsira anthu, yatumizidwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo mosakayikira, iwo adzaimvetsera.”+
16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+