Mateyu 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’malomwake, nthawi zonse muzipita kwa nkhosa zosochera za nyumba ya Isiraeli.+ Machitidwe 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba anamutumiza kwa inu,+ kuti adzakudalitseni mwa kubweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.” Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+
26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba anamutumiza kwa inu,+ kuti adzakudalitseni mwa kubweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.”
16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+