-
Nehemiya 5:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kuwonjezera apo, ndinakutumula zovala zanga, kenako ndinati: “Mofanana ndi zimenezi, Mulungu woona akutumule munthu aliyense wosachita mogwirizana ndi mawu amenewa, kum’chotsa m’nyumba yake ndi pa zinthu zake zonse. Ndipo munthu wotero akutumulidwe mwa njira imeneyi ndi kukhala wopanda kalikonse.” Pamenepo mpingo wonse unati: “Zikhale momwemo!”*+ Ndipo anayamba kutamanda Yehova.+ Choncho anthuwo anachitadi mogwirizana ndi mawu amenewa.+
-