1 Samueli 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+ 1 Petulo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+
10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+
14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+