1 Petulo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinu osangalala*+ ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu chifukwa zimenezi zikusonyeza kuti mzimu woyera wa Mulungu komanso ulemerero wake zili pa inu. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2014, tsa. 32
14 Ndinu osangalala*+ ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu chifukwa zimenezi zikusonyeza kuti mzimu woyera wa Mulungu komanso ulemerero wake zili pa inu.