Yakobo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wosangalala ndi munthu amene akupirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ imene Yehova* analonjeza onse amene akupitiriza kumukonda.+ Yakobo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawaona kuti ndi odala.*+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mukudziwa madalitso amene Yehova* anamupatsa.+ Mukuona nokha kuti Yehova* ndi wachikondi chachikulu komanso wachifundo.+
12 Wosangalala ndi munthu amene akupirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ imene Yehova* analonjeza onse amene akupitiriza kumukonda.+
11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawaona kuti ndi odala.*+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mukudziwa madalitso amene Yehova* anamupatsa.+ Mukuona nokha kuti Yehova* ndi wachikondi chachikulu komanso wachifundo.+