2 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Panopa andisungira chisoti chachifumu cha olungama.+ Ambuye, woweruza wachilungamo,+ adzandipatsa mphotoyi pa tsikulo.+ Sikuti adzapatsa ine ndekha, koma adzapatsanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere. 1 Petulo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo mʼbusa wamkulu+ akadzaonekera, mudzalandira mphoto* yosawonongeka yomwe ndi yaulemerero.+ Chivumbulutso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi apitiriza kuponya mʼndende ena a inu kuti muyesedwe mpaka pamapeto, ndipo mudzakhala mʼmasautso kwa masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+
8 Panopa andisungira chisoti chachifumu cha olungama.+ Ambuye, woweruza wachilungamo,+ adzandipatsa mphotoyi pa tsikulo.+ Sikuti adzapatsa ine ndekha, koma adzapatsanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere.
10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi apitiriza kuponya mʼndende ena a inu kuti muyesedwe mpaka pamapeto, ndipo mudzakhala mʼmasautso kwa masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+