Machitidwe 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko ansembe aakulu ndi amuna olemekezeka pakati pa Ayuda anamuuza zambiri+ zoneneza Paulo. Ndiyeno anayamba kumuchonderera, Machitidwe 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo pamene ndinali ku Yerusalemu, ansembe aakulu komanso akulu a Ayuda anabwera kudzamuneneza.+ Anali kupempha kuti apatsidwe chiweruzo chakuti aphedwe.
2 Kumeneko ansembe aakulu ndi amuna olemekezeka pakati pa Ayuda anamuuza zambiri+ zoneneza Paulo. Ndiyeno anayamba kumuchonderera,
15 ndipo pamene ndinali ku Yerusalemu, ansembe aakulu komanso akulu a Ayuda anabwera kudzamuneneza.+ Anali kupempha kuti apatsidwe chiweruzo chakuti aphedwe.