Machitidwe 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita masiku asanu, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula, dzina lake Teritulo. Iwo ananeneza+ Paulo kwa bwanamkubwa.+ Machitidwe 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo pamene ndinali ku Yerusalemu, ansembe aakulu komanso akulu a Ayuda anabwera kudzamuneneza.+ Anali kupempha kuti apatsidwe chiweruzo chakuti aphedwe.
24 Patapita masiku asanu, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula, dzina lake Teritulo. Iwo ananeneza+ Paulo kwa bwanamkubwa.+
15 ndipo pamene ndinali ku Yerusalemu, ansembe aakulu komanso akulu a Ayuda anabwera kudzamuneneza.+ Anali kupempha kuti apatsidwe chiweruzo chakuti aphedwe.