Yesaya 48:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sonkhanani pamodzi nonsenu ndipo mumvetsere. Ndi ndani pakati pawo amene walengeza zinthu zimenezi? Yehova wamukonda.+ Adzachitira Babulo zimene akufuna,+Ndipo dzanja lake lidzaukira Akasidi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:14 Yesaya 2, tsa. 130
14 Sonkhanani pamodzi nonsenu ndipo mumvetsere. Ndi ndani pakati pawo amene walengeza zinthu zimenezi? Yehova wamukonda.+ Adzachitira Babulo zimene akufuna,+Ndipo dzanja lake lidzaukira Akasidi.+