Hoseya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ndiyeno ana a Isiraeli adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene anali kuuzidwa kuti, ‘Anthu inu sindinu anthu anga,’+ adzauzidwanso kuti, ‘Inu ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+ Agalatiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma nonsenu ndinu ana+ a Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu.
10 “Ndiyeno ana a Isiraeli adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene anali kuuzidwa kuti, ‘Anthu inu sindinu anthu anga,’+ adzauzidwanso kuti, ‘Inu ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+